Psalms 35:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta, Mulungu wanga, chifukwa cha kulungama kwanu, onetsani kuti ine ndine wosalakwa, ndipo musalole kuti adani anga akondwere chifukwa cha mavuto anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundiweruze monga mwa chilungamo chanu, Yehova Mulungu wanga; ndipo asandisekerere ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onetsani kusalakwa kwanga mwa chilungamo chanu, Inu Yehova Mulungu wanga. Musalole kuti akondwere chifukwa cha mavuto anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundiweruze monga mwa cilungamo canu, Yehova Mulungu wanga; Ndipo asandisekerere ine.