Psalms 35:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tengani mkondo ndi nthungo, kuti mulimbane nawo anthu ondilondola. Uzani mtima wanga kuti, “Mpulumutsi wako ndine.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sololani nthungo, ndipo muwatsekerezere kunjira akundilondola. Nenani ndi moyo wanga, Chipulumutso chako ndine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tengani mkondo ndi nthungo, kulimbana ndi iwo amene akundithamangitsa. Uzani moyo wanga kuti, “Ine ndine chipulumutso chako.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sololani nthungo, ndipo muwatsekerezere kunjira akundilondola: Nenani ndi moyo wanga, Cipulumutso cako ndine.