Psalms 35:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anyozeke ndi kuchita manyazi onse ofunafuna moyo wanga. Abwezeni m'mbuyo ndipo athaŵe chinambalala amene apangana kuti andichite choipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Athe nzeru nachite manyazi iwo akufuna moyo wanga; abwezedwe m'mbuyo nasokonezeke iwo akundipangira chiwembu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene akufunafuna moyo wanga anyozedwe ndi kuchita manyazi; iwo amene akukonza kuti moyo wanga uwonongeke abwerere mʼmbuyo mochititsa mantha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Athe nzeru nacite manyazi iwo akufuna moyo wanga: Abwezedwe m'mbuyo nasokonezeke iwo akundipangira ciwembu.