Psalms 35:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akhale ngati mankhusu ouluka ndi mphepo, pamene mngelo wa Chauta akuŵapirikitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akhale monga mungu kumphepo, ndipo mngelo wa Yehova awapirikitse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akhale ngati mankhusu owuluka ndi mphepo pamene mngelo wa Yehova akuwapirikitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akhale monga mungu kumphepo, Ndipo mngelo wa Yehova awapitikitse.