Psalms 35:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adaniwo adanditchera ukonde popanda chifukwa, adandikumbira mbuna ine munthu wosachimwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ananditchera ukonde wao m'mbunamo kopanda chifukwa, anakumbira moyo wanga dzenje kopanda chifukwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Popeza ananditchera ukonde popanda chifukwa ndipo popanda chifukwa andikumbira dzenje,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti anandichera ukonde wao m'mbunamo kopanda cifukwa, Anakumbira moyo wanga dzenje kopanda cifukwa.