Psalms 36:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalole kuti mapazi a anthu odzikuza andipondereze, ndipo kuti manja a anthu oipa andipirikitse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Phazi la akudzikuza lisandifikire ine, ndi dzanja la oipa lisandichotse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musalole kuti phazi la wodzikuza libwere kulimbana nane, kapena dzanja la oyipa kundithamangitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Phazi la akudzikuza lisandifikire ine, Ndi dzanja la oipa lisandicotse.