Psalms 36:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amadzinyenga m'maganizo mwake, kotero kuti tchimo lake sangathe kulizindikira ndi kudana nalo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti adzidyoletsa yekha m'kuona kwake, kuti anthu sadzachipeza choipa chake ndi kukwiya nacho.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti iye mʼkuona kwake amadzinyenga yekha kwambiri, sazindikira kapena kudana ndi tchimo lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakud adzidyoletsa yekha m'kuona kwace, Kuti anthu sadzacipeza coipa cace ndi kukwiya naco.