Psalms 36:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mau a pakamwa pake ndi oipa ndi onyenga. Sachita zanzeru kapena zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mau a pakamwa pake ndiwo opanda pake ndi onyenga, waleka kuzindikira ndi kuchita bwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mawu a pakamwa pake ndi oyipa ndi achinyengo; iyeyo waleka kukhala wanzeru ndi kuchita zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mau a pakamwa pace ndiwo opanda pace ndi onyenga: Waleka kuzindikira ndi kucita bwino.