Psalms 36:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Chauta, chikondi chanu chosasinthika chimafika mpaka kumwamba, kukhulupirika kwanu kumafika mpaka ku mitambo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, m'mwamba muli chifundo chanu; choonadi chanu chifikira kuthambo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondi chanu Yehova, chimafika ku mayiko a kumwamba, kukhulupirika kwanu mpaka ku mitambo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, m'mwambamuli cifundo canu; Coonadi canu cifikira kuthambo.