Psalms 36:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chikondi chanu chosasinthika ndi chamtengowapatali. Nchifukwa chake anthu anu amathaŵira m'munsi mwa mapiko anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ha! Chifundo chanu, Mulungu, nchokondedwadi! Ndipo ana a anthu athawira kumthunzi wa mapiko anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chikondi chanu chosatha ndi chamtengowapatali! Otchuka pamodzi ndi anthu wamba pakati pa anthu amapeza pothawirapo mu mthunzi wa mapiko anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ha! cifundo canu, Mulungu, ncokondedwadi! Ndipo ana a anthu athawira ku mthunzi wa mapiko anu.