Psalms 36:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mumaŵadyetsa zonona m'nyumba mwanu, ndipo mumaŵamwetsa madzi a mu mtsinje wa madalitso anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Adzakhuta kwambiri ndi zonona za m'nyumba mwanu, ndipo mudzawamwetsa mu mtsinje wa zokondweretsa zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amadyerera zinthu zambiri za mʼnyumba yanu; Inu mumawapatsa chakumwa kuchokera mu mtsinje wanu wachikondwerero.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Adzakhuta kwambiri ndi zonona za m'nyumba mwanu: Ndipo mudzawamwetsa mu mtsinje wa zokondweretsa zanu.