Psalms 36:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kwa Inu kuli kasupe wamoyodi, m'kuŵala kwanu ifenso timaona kuŵala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti chitsime cha moyo chili ndi Inu, M'kuunika kwanu tidzaona kuunika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti kwa Inu kuli kasupe wamoyo; mʼkuwala kwanu ifenso timaona kuwala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti citsime ca moyo ciri ndi Inu: M'kuunika kwanu tidzaona kuunika.