Psalms 37:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usamavutika ndi anthu oipa. Usamakhumbira kukhala ngati ochita zoipa,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Salimo la Davide. Usavutike mtima chifukwa cha ochita zoipa, usachite nsanje chifukwa cha ochita chosalungama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Salimo la Davide. Usamavutike chifukwa cha anthu oyipa kapena kuchitira nsanje amene akuchita cholakwa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usabvutike mtima cifukwa ca ocita zoipa, Usacite nsanje cifukwa ca ocita cosalungama.