Psalms 37:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu ofatsa adzalandira dziko kuti likhale lao, ndipo adzakhala pa mtendere wosaneneka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ofatsa adzalandira dziko lapansi; nadzakondwera nao mtendere wochuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ofatsa adzalandira dziko ndipo adzasangalala ndi mtendere waukulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ofatsa adzalandira dziko lapansi; Nadzakondwera nao mtendere wocuruka.