Psalms 37:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu woipa amachitira upo mnzake wabwino, namamtuzulira maso mwachidani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Woipa apangira chiwembu wolungama, namkukutira mano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oyipa amakonza chiwembu kutsutsana ndi olungama ndipo amawakukutira mano;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Woipa apangira ciwembu wolungama, Namkukutira mano.