Psalms 37:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu oipa amasolola lupanga, ndipo amakoka mauta, kuti aphe anthu ovutika ndi osoŵa, amene amayenda molungama.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; alikhe ozunzika ndi aumphawi, aphe amene ali oongoka m'njira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Oyipa amasolola lupanga ndi kupinda uta kugwetsa osauka ndi osowa, kupha iwo amene njira zawo ndi zolungama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Oipa anasolola lupanga, nakoka uta wao; Alikhe ozunzika ndi aumphawi, Aphe amene ali oongoka m'njira: