Psalms 37:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nkwabwino kukhala m'chilungamo ndi kusauka, kupambana kukhala nazo zokoma zambiri zimene munthu woipa ali nazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zochepa zake za wolungama zikoma koposa kuchuluka kwao kwa oipa ambiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zabwino zochepa zimene olungama ali nazo ziposa chuma cha anthu oyipa ambiri;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zocepa zace za wolungama zikoma Koposa kucuruka kwao kwa oipa ambiri.