Psalms 37:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amasamalira moyo wa anthu angwiro, ndipo choloŵa chao chidzakhalapo mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova adziwa masiku a anthu angwiro; ndipo chosiyira chao chidzakhala chosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Masiku a anthu osalakwa amadziwika ndi Yehova, ndipo cholowa chawo chidzakhala mpaka muyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova adziwa masiku a anthu angwiro: Ndipo cosiyira cao cidzakhala cosatha.