Psalms 37:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa nthaŵi ya mavuto sadzazunzika, pa nthaŵi yanjala, adzakhala nazo zakudya zochuluka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sadzachita manyazi m'nyengo yoipa, ndipo m'masiku a njala adzakhuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa nthawi ya mavuto iwo sadzafota; mʼmasiku a njala adzakhala ndi zinthu zambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sadzacita manyazi m'nyengo yoipa: Ndipo m'masiku a njala adzakhuta.