Psalms 37:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti mosachedwa amanyala ngati udzu, ndipo amafota ngati masamba aaŵisi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti adzawamweta msanga monga udzu, ndipo adzafota monga msipu wauwisi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pakuti monga udzu iwo adzafota msanga, ngati mbewu zobiriwira adzanyala msanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti adzawamweta msanga monga udzu, Ndipo adzafota monga msipu wauwisi.