Psalms 37:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu oipa amatha. Adani a Chauta amafota ngati maluŵa, amazimirira ngati utsi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti oipa adzatayika, ndipo adani ake a Yehova adzanga mafuta a anaankhosa; adzanyeka, monga utsi adzakanganuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma oyipa adzawonongeka; adani a Yehova adzakhala ngati kukongola kwa kuthengo, iwo adzazimirira ngati utsi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti oipa adzatayika, Ndipo adani ace a Yehova adzanga mafuta a ana a nkhosa: Adzanyeka, monga utsi adzakanganuka.