Psalms 37:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene Chauta adaŵadalitsa, adzalandira dziko kuti likhale lao, koma amene Chauta adaŵatemberera adzaonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti iwo amene awadalitsa adzalandira dziko lapansi; koma iwo amene awatemberera adzadulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene Yehova amawadalitsa adzalandira dziko, koma amene Iye amawatemberera adzachotsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti iwo amene awadalitsa adzalandira dziko lapansi; Koma iwo amene awatemberera adzadulidwa.