Psalms 37:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngakhale agwe sadzapweteka, popeza kuti Chauta amamgwira dzanja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Angakhale akagwa, satayikiratu, pakuti Yehova agwira dzanja lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ngakhale atapunthwa sadzagwa, pakuti Yehova amamutchinjiriza ndi dzanja lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Angakhale akagwa, satayikiratu: Pakuti Yehova agwira dzanja lace.