Psalms 37:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu a Mulungu adzalandira dziko kuti likhale lao, ndipo adzakhala m'menemo mpaka muyaya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Olungama adzalandira dziko lapansi, nadzakhala momwemo kosatha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
olungama adzalandira dziko ndipo adzakhazikikamo kwamuyaya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Olungama adzalandira dziko lapansi, Nadzakhala momwemo kosatha.