Psalms 37:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma wolungamayo Chauta sadzamsiya yekha m'manja mwa mdani wake, sadzalola kuti pomuweruza, mlandu wake umuipire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova sadzamsiya m'dzanja lake; ndipo sadzamtsutsa poweruzidwa iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma Yehova sadzawasiya pansi pa mphamvu yawo kapena kuti atsutsidwe pamene abweretsedwa pa milandu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova sadzamsiya m'dzanja lace: Ndipo sadzamtsutsa poweruzidwa iye.