Psalms 37:34 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Khulupirira Chauta, ndipo usunge njira zake. Motero adzakukweza ndipo udzalandira dziko kuti likhale lako. Udzaona anthu oipa akuwonongeka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yembekeza Yehova, nusunge njira yake, ndipo Iye adzakukweza kuti ulandire dziko. Pakudulidwa oipa udzapenya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khulupirira Yehova, ndipo sunga njira yake; Iye adzakukweza ndipo udzalandira dziko kuti likhale lako; udzaona anthu oyipa akuwonongeka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yembekeza Yehova, nusunge njira yace, Ndipo Iye adzakukweza kuti ulandire dziko: Pakudutidwa oipa udzapenya,