Psalms 37:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidaona munthu woipa akunyada ndi kudzitukumula ngati mkungudza wa ku Lebanoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndapenya woipa, alikuopsa, natasa monga mtengo wauwisi wanzika.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndinaona munthu woyipa ndi munthu wopanda chifundo akupeza bwino ngati mtengo wobiriwira pa nthaka ya makolo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndapenya woipa, alikuopsa, Natasa monga mtengo wauwisi wanzika.