Psalms 37:38 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu ochimwa adzaonongekeratu kwathunthu, iwo pamodzi ndi zidzukulu zao zomwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma olakwa adzaonongeka pamodzi; matsiriziro a oipa adzadulidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma anthu ochimwa adzawonongeka; iwowo pamodzi ndi zidzukulu zawo zomwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma olakwa adzaonongeka pamodzi: Matsiriziro a oipa adzadutidwa.