Psalms 37:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amaŵathandiza ndi kuŵalanditsa. Amaŵachotsa m'manja mwa anthu oipa nkuŵapulumutsa, popeza kuti anthuwo amadalira Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova awathandiza, nawalanditsa; awalanditsa kwa oipa nawapulumutsa, chifukwa kuti anamkhulupirira Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova amawathandiza ndi kuwalanditsa; Iye amawalanditsa kwa oyipa ndi kuwapulumutsa, pakuti amathawira kwa Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova awathandiza, nawalanditsa: Awalanditsa kwa oipa nawapulumutsa, Cifukwa kuti anamkhulupirira Iye,