Psalms 37:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adzaonetsa poyera kusalakwa kwako, ndipo kulungama kwako kudzaŵala ngati usana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzaonetsa chilungamo chako monga kuunika, ndi kuweruza kwako monga usana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye adzachititsa chilungamo chako kuwala ngati mʼbandakucha, chiweruzo chako ngati dzuwa la masana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzaonetsa cilungamo cako monga kuunika, Ndi kuweruza kwako monga usana.