Psalms 38:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukugunda, mphamvu zandithera, ndipo sindikutha kupenya bwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga ugundagunda, mphamvu yanga yachoka, ndipo kuunika kwa maso anga, ndi iko komwe kwandichokera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga ukugunda, mphamvu zanga zikutha; ngakhale kuwala kwachoka mʼmaso mwanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga ugundagunda, mphamvu yanga yacoka: Ndipo kuunika kwa maso anga, ndi iko komwe kwandicokera.