Psalms 38:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndili ngati gonthi, sindikumvako, ndili ngati mbeŵeŵe amene satha kulankhula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine, monga gonthi, sindimva; ndipo monga munthu wosalankhula, sinditsegula pakamwa panga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndili ngati munthu wosamva amene sangamve, monga wosayankhula, amene sangathe kutsekula pakamwa pake;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine, monga gonthi, sindimva; Ndipo monga munthu wosalankhula, sinditsegula pakamwa panga.