Psalms 38:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inde ndili ngati munthu amene saamva, chifukwa sindingathe kuyankhapo kanthu, pamene akundilankhula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inde ndikunga munthu wosamva, ndipo m'kamwa mwanga mulibe makani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndakhala ngati munthu amene samva, amene pakamwa pake sipangathe kuyankha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inde ndikunga munthu wosamva, Ndipo m'kamwa mwanga mulibe makani.