Psalms 38:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Popeza ndimapemphera kuti, “Musalole konse kuti akondwerere pa ine, amene amandinyodola akaona kuti ndikuterereka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndinati, Asakondwerere ine; pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti Ine ndinati, “Musawalole kuti akondwere kapena kudzikweza okha pa ine pamene phazi langa laterereka.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndinati, Asakondwerere ine: Pakuterereka phazi langa, asadzikuze pa ine.