Psalms 38:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inde, ndili pafupi kugwa, ndipo ndikumva kuŵaŵa nthaŵi zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndafikana potsimphina, ndipo chisoni changa chili pamaso panga chikhalire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndili pafupi kugwa, ndipo ndikumva kuwawa nthawi zonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndafikana potsimphina; Ndipo cisoni canga ciri pamaso panga cikhalire.