Psalms 38:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikuvomera kuipa kwanga, ndikuda nkhaŵa chifukwa cha machimo anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga; nditenga nkhawa chifukwa cha tchimo langa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikuvomereza mphulupulu zanga; ndipo ndavutika ndi tchimo langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga; Nditenga nkhawa cifukwa ca chimo langa.