Psalms 38:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ngamphamvu adani amene amafuna moyo wanga, ngambiri amene amandida popanda chifukwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma adani anga ali ndi moyo, nakhala ndi mphamvu, ndipo akundida kopanda chifukwa achuluka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambiri ndi adani anga amphamvu; amene amandida popanda chifukwa alipo ochuluka kwambiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma adani anga ali ndi moyo, nakhalandi mphamvu: Ndipo akundida kopanda cifukwa acuruka.