Psalms 38:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mivi yanu yandilasa, ndipo dzanja lanu landipsinja.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mivi yanu yandilowa, ndi dzanja lanu landigwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mivi yanu yandilasa, ndipo dzanja lanu latsika ndipo landifikira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mibvi yanu yandilowa, Ndi dzanja lanu landigwera.