Psalms 38:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu amene amandibwezera zoipa m'malo mwa zabwino ndiwo adani anga, chifukwa ine ndimachita zabwino.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo akubwezera choipa pa chabwino atsutsana nane, popeza nditsata chabwino.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene amandibwezera zoyipa mʼmalo mwa zabwino amandinyoza pamene nditsatira zabwino.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo akubwezera coipa pa cabwino Atsutsana nane, popeza nditsata cabwino.