Psalms 38:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thupi langa lilibe mphamvu chifukwa cha ukali wanu. M'nkhongono mwanga mwalobodoka chifukwa cha uchimo wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mumnofu mwanga mulibe chamoyo chifukwa cha ukali wanu; ndipo m'mafupa anga simuzizira, chifukwa cha cholakwa changa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha ukali wanu mulibe thanzi mʼthupi langa; mafupa anga alibe mphamvu chifukwa cha tchimo langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mumnofu mwanga mulibe camoyo cifukwa ca ukali wanu; Ndipo m'mafupa anga simuzizira, cifukwa ca colakwa canga.