Psalms 38:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Machimo anga andimiza msinkhu, akundilemera ngati katundu woposa mphamvu zanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mphulupulu zanga zapitirira pamutu panga; ndathodwa nazo monga ndi katundu wolemera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kulakwa kwanga kwandipsinja ngati katundu wolemera kwambiri kuposa mphamvu zanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mphulupulu zanga zapitirira pamutu panga: Ndathodwa nazo monga ndi katundu wolemera.