Psalms 38:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mabala anga aola ndipo akununkha chifukwa cha kupusa kwanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mabala anga anunkha, adaola, chifukwa cha kupusa kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mabala anga akuwola ndipo akununkha chifukwa cha uchitsiru wa moyo wanga wauchimo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mabala anga anunkha, adaola, Cifukwa ca kupusa kwanga.