Psalms 38:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Thupi langa likutentha kwambiri ndi malungo, ndipo lilibe nyonga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti m'chuuno mwanga mutentha kwambiri; palibe pamoyo m'mnofu mwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Msana wanga wagwidwa ndi ululu wosasimbika, mulibe thanzi mʼthupi langa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti m'cuuno mwanga mutentha kwambiri; Palibe pamoyo m'mnofu mwanga,