Psalms 38:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndatheratu, ndipo ndatswanyika. Ndikubuula chifukwa cha kuvutika mu mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndafooka ine, ndipo ndachinjizidwa, ndabangula chifukwa cha kumyuka mtima wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndilibe mphamvu ndipo ndakunthidwa kwathunthu; ndikubuwula ndi ululu wa mumtima.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndafoka ine, ndipo ndacinjizidwa: Ndabangula cifukwa ca kumyuka mtima wanga.