Psalms 38:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye, mumadziŵa zonse zimene ndimakhumba, kusisima kwanga sikuli kosamveka kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye, chikhumbo changa chonse chili pamaso panu; ndipo kubuula kwanga sikubisika kwa Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zokhumba zanga zonse zili poonekera pamaso panu Ambuye, kusisima kwanga sikunabisike kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye, cikhumbo canga conse ciri pamaso panu; Ndipo kubuula kwanga sikubisika kwa Inu.