Psalms 39:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musandiyang'ane mwaukali, choncho ndidzatha kusangalala, ndisanafe ndi kuzimirira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndiloleni, kuti nditsitsimuke, ndisanamuke ndi kukhala kuli zii.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musandiyangʼane mwaukali, choncho ndidzatha kusangalala ndisanafe ndi kuyiwalika.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndiloleni, kuti nditsitsimuke, Ndisanamuke ndi kukhala kuli zi.