Psalms 39:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero ndidakhala chete osalankhula kanthu, ndidakhala duu, koma popanda phindu, chifukwa mavuto anga ankangokulirakulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndinatonthola osanena mau, ndinakhala chete osalawa chokoma; ndipo chisoni changa chinabuka.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma pamene ndinali chete osanena ngakhale kanthu kalikonse kabwino mavuto anga anachulukirabe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndinatonthola osanena mau, ndinakhala cete osalawa cokoma; Ndipo cisoni canga cinabuka.