Psalms 39:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga udavutika, ndipo pamene ndidasinkhasinkha, mtima wanga udangoyaka moto. Pompo ndidalankhula ndi mau akuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima wanga unatentha m'kati mwa ine; unayaka moto pakulingirira ine. Pamenepo ndinalankhula ndi lilime langa,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wanga unatentha mʼkati mwanga, ndipo pamene ndinkalingalira, moto unayaka; kenaka ndinayankhula ndi lilime langa:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima wanga unatentha m'kati mwaine; Unayaka moto pakulingirira ine: Pamenepo ndinalankhula ndi lilime langa: