Psalms 39:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Inu Chauta, mundidziŵitse mathero a moyo wanga, mundidziŵitse kuchepa kwa masiku anga. Mundilangize kuti moyo wanga sukhalira kutha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova, mundidziwitse chimaliziro changa, ndi mawerengedwe a masiku anga ndi angati; ndidziwe malekezero anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yehova ndionetseni mathero a moyo wanga ndi chiwerengero cha masiku anga; mundidziwitse kuti moyo wanga ndi wosakhalitsa motani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova, mundidziwitse cimariziro canga, Ndi mawerengedwe a masiku anga ndi angati; Ndidziwe malekezero anga,