Psalms 39:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Onani, mwandipatsa masiku ochepa chabe, nthaŵi ya moyo wanga siili kanthu pamaso panu. Ndithudi, munthu aliyense ndi mpweya chabe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja; ndipo zaka zanga zili ngati chabe pamaso panu, Indedi munthu aliyense angakhale wokhazikika, ali chabe konse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu mwachititsa kuti masiku anga akhale ochepa kwambiri, kutalika kwa zaka zanga ndi kopanda phindu pamaso panu; moyo wa munthu aliyense ndi waufupi. Sela
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Onani, munaika masiku anga akhale monga kuyesa dzanja; Ndipo zaka zanga ziri ngati cabe pamaso panu: Indedi munthu ali yense angakhale wokhazikika, ali cabe konse.